Amalume Chifundo Ineh, mu mutima Aba ni a ndzanga Si ndiziba chifukwa Simu akondela Amalume Chifundo Ine, mu mutima Ala ni chete Asiyeni mu Mu asiye chon cho Ndichani Mu ni uze Chifukwa cha che Amalume Ndichani Simu kondela a ndzanga Aba ineh ni a ndzanga Kuchockela napamene Ineh ndinali mu ngono Ni nali usebela na a ndzanga Chifukwa cha che Ineh sindichiziba Mu ndi uzebo amalume